1 Mbiri 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa tsiku limenelo, iwo anadya ndi kumwa mosangalala kwambiri pamaso pa Yehova.+ Kachiwirinso, analonga Solomo mwana wa Davide kukhala mfumu,+ ndi kum’dzoza pamaso pa Yehova kukhala mtsogoleri.+ Anadzozanso Zadoki+ kukhala wansembe.
22 Pa tsiku limenelo, iwo anadya ndi kumwa mosangalala kwambiri pamaso pa Yehova.+ Kachiwirinso, analonga Solomo mwana wa Davide kukhala mfumu,+ ndi kum’dzoza pamaso pa Yehova kukhala mtsogoleri.+ Anadzozanso Zadoki+ kukhala wansembe.