1 Mbiri 29:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Akalonga onse+ ndi amuna amphamvu,+ ndiponso ana onse a Mfumu Davide,+ anali kugonjera Solomo mfumu.
24 Akalonga onse+ ndi amuna amphamvu,+ ndiponso ana onse a Mfumu Davide,+ anali kugonjera Solomo mfumu.