1 Mbiri 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova anapitiriza kukweza Solomo+ pamaso pa Aisiraeli onse, ndi kum’patsa ulemu waukulu wachifumu kuposa mfumu ina iliyonse imene inalamulira Isiraeli iye asanakhale mfumu.+
25 Yehova anapitiriza kukweza Solomo+ pamaso pa Aisiraeli onse, ndi kum’patsa ulemu waukulu wachifumu kuposa mfumu ina iliyonse imene inalamulira Isiraeli iye asanakhale mfumu.+