2 Mbiri 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Ataliya,+ mayi wa Ahaziya ataona kuti mwana wake wafa, anapha ana onse achifumu a nyumba ya Yuda.+
10 Kenako Ataliya,+ mayi wa Ahaziya ataona kuti mwana wake wafa, anapha ana onse achifumu a nyumba ya Yuda.+