11 Kenako anatulutsa mwana wa mfumu uja.+ Atatero anamuveka chisoti chachifumu+ n’kuika mpukutu wa Chilamulo cha Mulungu pamutu pake.+ Chotero anamulonga ufumu, ndipo Yehoyada ndi ana ake anamudzoza+ n’kuyamba kunena kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”+