2 Mbiri 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu ogwira ntchitowo anayamba ntchito yawo+ ndipo ntchito yokonza nyumbayo inali kuyenda bwino. Pomaliza pake anakonza nyumba ya Mulungu woona kuti ikhale mmene inayenera kukhalira ndipo anailimbitsa.
13 Anthu ogwira ntchitowo anayamba ntchito yawo+ ndipo ntchito yokonza nyumbayo inali kuyenda bwino. Pomaliza pake anakonza nyumba ya Mulungu woona kuti ikhale mmene inayenera kukhalira ndipo anailimbitsa.