2 Mbiri 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atsogoleri amenewa ankayang’anira gulu lankhondo la asilikali 307,500, omenya nkhondo mwamphamvu pothandiza mfumu kulimbana ndi adani.+
13 Atsogoleri amenewa ankayang’anira gulu lankhondo la asilikali 307,500, omenya nkhondo mwamphamvu pothandiza mfumu kulimbana ndi adani.+