2 Mbiri 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno mpingo wonsewo unagwirizana+ kuti uchitenso phwandolo masiku ena 7.+ Choncho analichitanso masiku 7 mosangalala.
23 Ndiyeno mpingo wonsewo unagwirizana+ kuti uchitenso phwandolo masiku ena 7.+ Choncho analichitanso masiku 7 mosangalala.