2 Mbiri 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anachita zoyenera pamaso pa Yehova+ ndipo anayenda m’njira za Davide kholo lake.+ Sanapatukire mbali ya kudzanja lamanja kapena lamanzere.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:2 Nsanja ya Olonda,12/1/2005, tsa. 21
2 Iye anachita zoyenera pamaso pa Yehova+ ndipo anayenda m’njira za Davide kholo lake.+ Sanapatukire mbali ya kudzanja lamanja kapena lamanzere.+