-
2 Mbiri 34:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 “Pitani mukafunsire+ kwa Yehova m’malo mwa ineyo,+ ndiponso m’malo mwa anthu amene atsala mu Isiraeli ndi mu Yuda. Mukafunse zokhudza mawu a m’buku+ limene lapezekali, chifukwa mkwiyo wa Yehova+ umene akuyenera kutitsanulira ndi waukulu, popeza makolo athu sanasunge mawu a Yehova. Iwo sanachite zonse zimene zinalembedwa m’buku ili.”+
-