2 Mbiri 35:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Muime+ m’malo oyera potsatira magulu a nyumba ya makolo anu kuti mutumikire abale anu, ana a anthuwa, ndipo gulu lililonse la anthu likhale ndi gulu lake la Alevi+ loti liziwatumikira, losankhidwa potsatira makolo awo.+
5 Muime+ m’malo oyera potsatira magulu a nyumba ya makolo anu kuti mutumikire abale anu, ana a anthuwa, ndipo gulu lililonse la anthu likhale ndi gulu lake la Alevi+ loti liziwatumikira, losankhidwa potsatira makolo awo.+