2 Mbiri 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo anamaliza kukonzekera+ ndipo ansembe anaimirirabe+ m’malo awo,+ komanso Alevi anali m’magulu awo+ mogwirizana ndi lamulo la mfumu.+
10 Iwo anamaliza kukonzekera+ ndipo ansembe anaimirirabe+ m’malo awo,+ komanso Alevi anali m’magulu awo+ mogwirizana ndi lamulo la mfumu.+