2 Mbiri 35:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuwonjezera apo, anakonza nsembe zopsereza kuti azipereke kwa ana a anthuwo potsatira magulu+ a nyumba ya makolo awo,+ kuti ziperekedwe+ kwa Yehova mogwirizana ndi zimene zinalembedwa m’buku la Mose.+ Anachitanso chimodzimodzi ndi ng’ombe.
12 Kuwonjezera apo, anakonza nsembe zopsereza kuti azipereke kwa ana a anthuwo potsatira magulu+ a nyumba ya makolo awo,+ kuti ziperekedwe+ kwa Yehova mogwirizana ndi zimene zinalembedwa m’buku la Mose.+ Anachitanso chimodzimodzi ndi ng’ombe.