Ezara 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma maso+ a Mulungu wawo anali+ pa akulu a Ayuda, ndipo anthu aja sanawasiyitse ntchitoyo. Anadikira mpaka pamene analemba chikalata chokhudza nkhaniyo n’kuchitumiza kwa Dariyo, ndiponso mpaka pamene chikalata choyankha nkhani imeneyi chinabwera. Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:5 Nsanja ya Olonda,2/1/1986, tsa. 291/15/1986, tsa. 29
5 Koma maso+ a Mulungu wawo anali+ pa akulu a Ayuda, ndipo anthu aja sanawasiyitse ntchitoyo. Anadikira mpaka pamene analemba chikalata chokhudza nkhaniyo n’kuchitumiza kwa Dariyo, ndiponso mpaka pamene chikalata choyankha nkhani imeneyi chinabwera.