Ezara 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Panalinso Zekariya kuchokera pa ana a Sekaniya, yemwe anali wochokera pa ana a Parosi.+ Iye anali ndi amuna amene analembetsa mayina awo okwanira 150.
3 Panalinso Zekariya kuchokera pa ana a Sekaniya, yemwe anali wochokera pa ana a Parosi.+ Iye anali ndi amuna amene analembetsa mayina awo okwanira 150.