-
Ezara 9:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 amene munatilamula kudzera mwa atumiki anu aneneri, akuti, ‘Dziko limene anthu inu mukukalitenga kukhala lanu ndi lodetsedwa chifukwa cha kudetsedwa kwa anthu a mitundu ina,+ ndiponso chifukwa cha zonyansa zawo+ zimene adzaza nazo dzikolo. Iwo adzaza dzikolo ndi zodetsa kuyambira koyambirira mpaka kumapeto.+
-