3 Tsopano tiyeni tichite pangano+ ndi Mulungu wathu, lakuti tisiya+ akazi onse amenewa ndi ana awo mogwirizana ndi lamulo la Yehova ndi la anthu amene akunjenjemera+ chifukwa cha lamulo+ la Mulungu wathu, kuti zinthu zichitike mogwirizana ndi lamulo.+