Ezara 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo Ezara ananyamuka ndipo anauza atsogoleri a ansembe, a Alevi ndi a Aisiraeli onse kuti alumbire+ kuti achita mogwirizana ndi mawu amenewa. Choncho iwo analumbira.
5 Pamenepo Ezara ananyamuka ndipo anauza atsogoleri a ansembe, a Alevi ndi a Aisiraeli onse kuti alumbire+ kuti achita mogwirizana ndi mawu amenewa. Choncho iwo analumbira.