Ezara 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ndi kuti aliyense amene sabwera+ potha masiku atatu mogwirizana ndi lamulo la akalonga+ ndi akulu, katundu wake yense alandidwa+ ndipo iyeyo achotsedwa+ pa khamu la anthu amene anachokera ku ukapolo.
8 ndi kuti aliyense amene sabwera+ potha masiku atatu mogwirizana ndi lamulo la akalonga+ ndi akulu, katundu wake yense alandidwa+ ndipo iyeyo achotsedwa+ pa khamu la anthu amene anachokera ku ukapolo.