Ezara 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Patapita nthawi wansembe Ezara anaimirira n’kuuza anthuwo kuti: “Inuyo mwachita zosakhulupirika chifukwa mwatenga akazi achilendo+ n’kuwonjezera pa machimo a Isiraeli.+
10 Patapita nthawi wansembe Ezara anaimirira n’kuuza anthuwo kuti: “Inuyo mwachita zosakhulupirika chifukwa mwatenga akazi achilendo+ n’kuwonjezera pa machimo a Isiraeli.+