-
Ezara 10:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Anthu amene anachokera ku ukapolowo+ anatsatira dongosolo limenelo, ndipo wansembe Ezara ndi amuna onse amene anali atsogoleri a nyumba za makolo awo,+ omwe anachita kuwatchula mayina awo, anachoka pakati pa anthuwo n’kukakhala pansi kuti afufuze nkhaniyo,+ kuyambira pa tsiku loyamba la mwezi wa 10.+
-