Ezara 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pomalizira pake, pofika pa tsiku loyamba la mwezi woyamba, anamaliza kufufuza amuna onse amene anatenga akazi achilendo.+
17 Pomalizira pake, pofika pa tsiku loyamba la mwezi woyamba, anamaliza kufufuza amuna onse amene anatenga akazi achilendo.+