Ezara 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma iwo analonjeza mwa kugwirana chanza kuti asiya akazi awo ndi kuti popeza anali atachimwa,+ nkhosa yamphongo iperekedwa+ chifukwa cha tchimo lawolo.
19 Koma iwo analonjeza mwa kugwirana chanza kuti asiya akazi awo ndi kuti popeza anali atachimwa,+ nkhosa yamphongo iperekedwa+ chifukwa cha tchimo lawolo.