Nehemiya 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Melatiya Mgibeoni+ ndi Yadoni Mmeronoti+ anakonza mpandawo kuchokera pamene Yoyada ndi Mesulamu analekezera. Amenewa anali amuna a ku Gibeoni+ ndi Mizipa+ amene anali pansi pa ulamuliro wa bwanamkubwa+ wa kutsidya la Mtsinje.+
7 Kenako Melatiya Mgibeoni+ ndi Yadoni Mmeronoti+ anakonza mpandawo kuchokera pamene Yoyada ndi Mesulamu analekezera. Amenewa anali amuna a ku Gibeoni+ ndi Mizipa+ amene anali pansi pa ulamuliro wa bwanamkubwa+ wa kutsidya la Mtsinje.+