Nehemiya 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma tinapemphera+ kwa Mulungu wathu, ndipo chifukwa cha adani amenewa, tinaika alonda kuti azititeteza usana ndi usiku.
9 Koma tinapemphera+ kwa Mulungu wathu, ndipo chifukwa cha adani amenewa, tinaika alonda kuti azititeteza usana ndi usiku.