Nehemiya 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno anthu a ku Yuda anayamba kunena kuti: “Mphamvu za anthu onyamula katundu+ zatha, koma pali zinyalala zambiri zofunika kuchotsa,+ ndipo ife sitingathe kumanga mpandawu tokha.”
10 Ndiyeno anthu a ku Yuda anayamba kunena kuti: “Mphamvu za anthu onyamula katundu+ zatha, koma pali zinyalala zambiri zofunika kuchotsa,+ ndipo ife sitingathe kumanga mpandawu tokha.”