Nehemiya 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho ndinaika amuna kuseli kwa mpanda pamalo otsika ndiponso oonekera. Ndinaikanso anthu onyamula malupanga,+ mikondo ing’onoing’ono+ ndi mauta malinga ndi mabanja awo.
13 Choncho ndinaika amuna kuseli kwa mpanda pamalo otsika ndiponso oonekera. Ndinaikanso anthu onyamula malupanga,+ mikondo ing’onoing’ono+ ndi mauta malinga ndi mabanja awo.