Nehemiya 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho ndinawatumizira amithenga+ kuti akawauze kuti: “Ntchito imene ndikugwirayi ndi yaikulu,+ sindingathe kupita kumeneko. Kodi ntchitoyi iime chifukwa chakuti ine ndabwera kwa inu?”+
3 Choncho ndinawatumizira amithenga+ kuti akawauze kuti: “Ntchito imene ndikugwirayi ndi yaikulu,+ sindingathe kupita kumeneko. Kodi ntchitoyi iime chifukwa chakuti ine ndabwera kwa inu?”+