-
Nehemiya 6:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndiyeno ine ndinalowa m’nyumba ya Semaya mwana wamwamuna wa Delaya, mwana wamwamuna wa Mehetabele, amene anali atadzitsekera m’nyumba.+ Iye anandiuza kuti: “Tipangane nthawi kuti tikakumane+ kunyumba ya Mulungu woona, m’kachisi,+ ndi kutseka zitseko za kachisiyo, pakuti akubwera kudzakupha, ngakhale usiku+ akubwera ndithu kudzakupha.”
-