Nehemiya 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komanso masiku amenewo, anthu olemekezeka+ a mu Yuda anali kulemberana makalata ambiri ndi Tobia.+
17 Komanso masiku amenewo, anthu olemekezeka+ a mu Yuda anali kulemberana makalata ambiri ndi Tobia.+