-
Nehemiya 8:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndiyeno Alevi anali kuuza anthu onse kuti akhale chete ndipo anati: “Khalani chete! pakuti lero ndi tsiku lopatulika, musadzimvere chisoni.”
-