Nehemiya 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo mbewu ya Isiraeli inadzipatula+ kwa anthu onse osakhala Aisiraeli.+ Atatero anaimirira ndi kuulula+ machimo awo+ ndi zolakwa za makolo awo.+
2 Pamenepo mbewu ya Isiraeli inadzipatula+ kwa anthu onse osakhala Aisiraeli.+ Atatero anaimirira ndi kuulula+ machimo awo+ ndi zolakwa za makolo awo.+