Nehemiya 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kuwonjezera apo, tinadziikira malamulo akuti chaka chilichonse aliyense wa ife azipereka gawo limodzi mwa magawo atatu a sekeli kuti ndalama zimenezo akazigwiritsire ntchito pa utumiki wa panyumba ya Mulungu wathu.+
32 Kuwonjezera apo, tinadziikira malamulo akuti chaka chilichonse aliyense wa ife azipereka gawo limodzi mwa magawo atatu a sekeli kuti ndalama zimenezo akazigwiritsire ntchito pa utumiki wa panyumba ya Mulungu wathu.+