-
Nehemiya 11:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Panalinso Maaseya mwana wa Baruki amene anali mwana wa Kolihoze. Kolihoze anali mwana wa Hazaya, Hazaya anali mwana wa Adaya, Adaya anali mwana wa Yoyaribi, Yoyaribi anali mwana wa Zekariya amene anali mwana wa Mshela.
-