7 Ana aamuna a Benjamini+ anali awa: Salelu mwana wa Mesulamu,+ Mesulamu anali mwana wa Yoedi, Yoedi anali mwana wa Pedaya, Pedaya anali mwana wa Kolaya, Kolaya anali mwana wa Maaseya, Maaseya anali mwana wa Itiyeli, ndipo Itiyeli anali mwana wa Yesaiya.