-
Nehemiya 11:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Mataniya+ mwana wa Mika amene anali mwana wa Zabidi mwana wa Asafu,+ anali wotsogolera nyimbo zotamanda+ Mulungu. Iye anali kutamanda Mulungu pa nthawi ya mapemphero.+ Bakibukiya anali wachiwiri kwa woyang’anira pakati pa abale ake. Panalinso Abada mwana wa Samuwa, Samuwa anali mwana wa Galali, ndipo Galali+ anali mwana wa Yedutuni.+
-