Nehemiya 12:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anthu amenewa anakhalapo m’masiku a Yoyakimu+ mwana wa Yesuwa+ amene anali mwana wa Yozadaki,+ komanso m’masiku a Nehemiya+ amene anali bwanamkubwa, ndi Ezara+ amene anali wansembe komanso wokopera Malemba.+
26 Anthu amenewa anakhalapo m’masiku a Yoyakimu+ mwana wa Yesuwa+ amene anali mwana wa Yozadaki,+ komanso m’masiku a Nehemiya+ amene anali bwanamkubwa, ndi Ezara+ amene anali wansembe komanso wokopera Malemba.+