Nehemiya 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno ansembe ndi Alevi anadziyeretsa+ ndi kuyeretsanso anthu,+ zipata+ ndi khoma la mpandawo.+