Nehemiya 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa tsiku limenelo buku+ la Mose linawerengedwa+ pamaso pa anthuwo. Iwo anapeza kuti m’bukumo analembamo kuti Muamoni+ ndi Mmowabu+ aliyense sayenera kubwera mumpingo wa Mulungu woona mpaka kalekale,+
13 Pa tsiku limenelo buku+ la Mose linawerengedwa+ pamaso pa anthuwo. Iwo anapeza kuti m’bukumo analembamo kuti Muamoni+ ndi Mmowabu+ aliyense sayenera kubwera mumpingo wa Mulungu woona mpaka kalekale,+