Nehemiya 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zitatero ndinalamula kuti ayeretse+ zipinda zodyeramo+ ndipo anachitadi zomwezo. Kenako ndinabwezera pamalo pake ziwiya+ za nyumba ya Mulungu woona pamodzi ndi zopereka zambewu ndi lubani.+
9 Zitatero ndinalamula kuti ayeretse+ zipinda zodyeramo+ ndipo anachitadi zomwezo. Kenako ndinabwezera pamalo pake ziwiya+ za nyumba ya Mulungu woona pamodzi ndi zopereka zambewu ndi lubani.+