Esitere 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno mfumu inavula mphete yake yodindira+ imene inalanda Hamani ndi kuipereka kwa Moredekai. Pamenepo Esitere anaika Moredekai kuti ayang’anire nyumba ya Hamani.+
2 Ndiyeno mfumu inavula mphete yake yodindira+ imene inalanda Hamani ndi kuipereka kwa Moredekai. Pamenepo Esitere anaika Moredekai kuti ayang’anire nyumba ya Hamani.+