Esitere 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakati pa Ayuda panali chisangalalo, kukondwa+ ndi kunyadira ndipo anthu anali kuwapatsa ulemu.