Esitere 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Izi zinali choncho chifukwa Moredekai anali ndi udindo waukulu+ m’nyumba ya mfumu ndipo anatchuka+ m’zigawo zonse chifukwa mphamvu zake zinali kukulirakulira.+
4 Izi zinali choncho chifukwa Moredekai anali ndi udindo waukulu+ m’nyumba ya mfumu ndipo anatchuka+ m’zigawo zonse chifukwa mphamvu zake zinali kukulirakulira.+