Esitere 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ayuda amene anali ku Susani anasonkhana pamodzi pa tsiku la 13+ ndi la 14 la mweziwo. Ndipo pa tsiku la 15 la mweziwo anapuma ndipo analisandutsa tsiku laphwando ndi lachikondwerero.+
18 Ayuda amene anali ku Susani anasonkhana pamodzi pa tsiku la 13+ ndi la 14 la mweziwo. Ndipo pa tsiku la 15 la mweziwo anapuma ndipo analisandutsa tsiku laphwando ndi lachikondwerero.+