Esitere 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 N’chifukwa chake Ayuda akumidzi amene anali kukhala m’madera akutali ndi mzinda, anasandutsa tsiku la 14 la mwezi wa Adara+ kukhala tsiku lachikondwerero,+ laphwando, losangalala ndiponso tsiku+ lotumizirana chakudya.+
19 N’chifukwa chake Ayuda akumidzi amene anali kukhala m’madera akutali ndi mzinda, anasandutsa tsiku la 14 la mwezi wa Adara+ kukhala tsiku lachikondwerero,+ laphwando, losangalala ndiponso tsiku+ lotumizirana chakudya.+