Esitere 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 N’chifukwa chake masiku amenewa anawatcha kuti Purimu, kutengera dzina la Puri.+ Choncho mogwirizana ndi mawu onse a m’kalata imeneyi+ komanso chifukwa cha zimene anaona pa nkhani imeneyi ndi zimene zinawachitikira,
26 N’chifukwa chake masiku amenewa anawatcha kuti Purimu, kutengera dzina la Puri.+ Choncho mogwirizana ndi mawu onse a m’kalata imeneyi+ komanso chifukwa cha zimene anaona pa nkhani imeneyi ndi zimene zinawachitikira,