Yobu 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ineyo ndaonapo wopusa akuzika mizu,+Koma mwadzidzidzi ndinayamba kutemberera malo ake okhala.