-
Yobu 5:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Pajatu zopweteka sizichokera m’fumbi,
Ndipo mavuto satuluka m’nthaka.
-
6 Pajatu zopweteka sizichokera m’fumbi,
Ndipo mavuto satuluka m’nthaka.