Yobu 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tamvera! N’ngodala munthu amene Mulungu amam’dzudzula,+Ndipo chilango* cha Wamphamvuyonse usachikane. Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:17 Nsanja ya Olonda,6/1/1993, tsa. 21
17 Tamvera! N’ngodala munthu amene Mulungu amam’dzudzula,+Ndipo chilango* cha Wamphamvuyonse usachikane.