-
Yobu 5:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Udzaona ndithu kuti mtendere ndiwo hema wako,
Ndipo ukapita kukayendera malo ako odyetserako ziweto, udzaona kuti palibe chimene chikusowa.
-